Skip navigation.

A Handbook for Community- Based Volunteers as Para-legals in Domestic Violence and HIV Prevention in Malawi

Publication year: 
2013
Series: 
UN Women
Abstract:

This training manual is available in English and Chichewa for Malawi (click on the links below to download English or Chichewa Manuals).

English:
The training manual is targeted at building requisite knowledge and skills
to make basic interpretation and application of relevant National legal and
policy instruments related to HIV and Domestic Violence Prevention amongst
Community-Based Volunteers (CBVs).

This course is targeted at providing CBVs, strategic government departments, traditional and religious leaders with basic legal skills that will enable them to contribute towards the following:
• Providing basic legal information and support to women and girls who are survivors of domestic violence
• Supporting traditional courts with relevant common law instruments they can consider when making judgments in domestic violence-related cases
• Strengthening the domestic violence referral system by creating linkages between traditional and common law referral points.

---------------------------------------------------------------------------------

Chichewa:
Cholinga cha phunzilo la mu bukhuli ndi kupereka upangili, luso ndi luntha
pankhani za malamulo ndi ndondomeko zokhudza kuthetsa HIV ndi nkhanza
za m’banja kwa alangizi a mmudzi (ma volontiya).

Bukhuli lapangidwa pofuna kupeleka luso ndi luntha kwa alangizi a mmidzi, atsogoleri a mmadera ndi atsogoleri a zipembedzo kuti athe kuthandizira pa nkhani izi:
• kupeleka uphungu ndi thandizo kwa amayi ndi atsikana amene akumana ndi nkhanza za m’banja.
• Kuthandizila ndi kuunikila ma khoti a ku mudzi pa nkhani za malamulo a dziko pomwe ma khothiwo afuna kupeleka chigamulo pa milandu yokhudzana ndi nkhanza za m’banja.
• Kulimbikitsa kunena za kuipa kwa nkhaza za m’banja kudzera mu kupanga malo omwe anthu angapeze thandizo pa za malamulo a boma ndi a chikhalidwe pa nkhani za nkhanza.